Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 26:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndidzacitira inu icinso; ndidzakuikirani zoopsa, nthendayoondetsayam'cifuwa ndi malungo, zakulanda maso ndi mphamvu, ndi kuzunza moyo; ndipo mudzabzala mbeu zanu cabe, pope za adani anu adzazidya.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 26

Onani Levitiko 26:16 nkhani