Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 25:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo uziwerengera masabata a zaka asanu ndi awiri, zaka zisanu ndi ziwiri kasanu ndi kawiri; kotero kuti zaka za masabata a zaka asanu ndi awiri, zifikire zaka makumi anai kudza zisanu ndi zinai.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 25

Onani Levitiko 25:8 nkhani