Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 25:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo sabata la dzikoli likhale kwa inu la cakudya; kwa iwe, ndi mnyamata wako, ndi mdzakazi wako, ndi wolembedwa nchito yako, ndi mlendo wako wakugonera kwanu;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 25

Onani Levitiko 25:6 nkhani