Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 25:47 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mlendo wakugonera kwanu akalemera cuma, ndi mbale wako wakukhala naye akasauka, nadzigulitsa kwa mlendo wakugonera kwanu, kapena kwa pfuko la banja la mlendo;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 25

Onani Levitiko 25:47 nkhani