Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 25:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akapanda kuiombola kufikira kutha kwace kwa caka camphumphu, nyumba iri m'mudzi wa m'lingayi idzakhala yace ya iye adaigula yosamcokeranso mwa mibadwo yace; siidzaturuka caka coliza lipenga.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 25

Onani Levitiko 25:30 nkhani