Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 25:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma dzanja lace likapanda kupeza zofikira za kumbwezera, pamenepo cogulitsaco cikhale m'dzanja lace la iye adacigulayo, kufikira caka coliza lipenga; koma caka coliza lipenga cituruke, nabwerere iye ku dziko lace.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 25

Onani Levitiko 25:28 nkhani