Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 24:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi iye wakucitira mwano dzina la Yehova, amuphe ndithu; khamu lonse limponye miyala ndithu; mlendo ndi wobadwa m'dziko yemwe akacitira dzina la Yehova mwano, awaphe.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 24

Onani Levitiko 24:16 nkhani