Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 23:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Izi ndi nyengo zoikika za Yehova, zimene muzilalikira zikhale masonkhano opatulika, kukabwera nayo nsembe yamoto kwa Yehova, nsembe yopsereza, ndi nsembe yaufa, nsembe yophera, ndi nsembe yothira, yonse pa tsiku lace lace;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 23

Onani Levitiko 23:37 nkhani