Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 23:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Komatu, tsiku lakhumi la mwezi uwu wacisanu ndi ciwiri, ndilo tsiku la citetezero; mukhale nao msonkhano wopatulika, ndipo mudzicepetse; ndi kubwera nayo nsembe yamoto kwa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 23

Onani Levitiko 23:27 nkhani