Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 23:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakukolola dzinthu za m'dziko mwanu, usamakololetsa m'mphepete mwa munda wako, nusamakunkha khunkha; uzisiyire wosauka ndi mlendo; Ine ndine Yehova Mulungu wako.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 23

Onani Levitiko 23:22 nkhani