Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 23:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti,

2. Nena ndi ana a Israyeli, nuti nao, Nyengo zoikika za Yehova zimene muzilalikira zikhale masonkhano opatulika, ndizo nyengo zanga zoikika.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 23