Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 22:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mwana wamkazi wa wansembe akakhala wamasiye kapena wocotsedwa, ndipo alibe mwana, nabwerera ku nyumba ya atate wace, monga muja anali mwana, adyeko mkate wa atate wace; koma mlendo asamadyako.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 22

Onani Levitiko 22:13 nkhani