Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 20:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero muzisunga malemba anga onse, ndi maweruzo anga onse, kuwacita; lingakusanzeni inu dziko limene ndipita nanuko, kuti mukhale m'mwemo.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 20

Onani Levitiko 20:22 nkhani