Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 2:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ukabwera naco copereka ndico nsembe yaufa, yophika mumcembo, cizikhala ca timitanda ta ufa wosalala topanda cotupitsa tosanganiza ndi mafuta, kapena timitanda taphanthi topanda cotupitsa todzoza ndi mafuta.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 2

Onani Levitiko 2:4 nkhani