Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 2:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munthu akabwera naco copereka ndico nsembe yaufa ya kwa Yehova, copereka cace cizikhala ca ufa wosalala; ndipo athirepo mafuta, ndi kuikapo libano.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 2

Onani Levitiko 2:1 nkhani