Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 19:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mlendo wakugonera kwa inu mumuyese pakati pa inu monga wa m'dziko momwemo; umkonde monga udzikonda wekha; popeza munali alendo m'dziko la Aigupto; Ine ndine Yehova Mulungu wanu.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 19

Onani Levitiko 19:34 nkhani