Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 19:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Muzisunga malemba anga, Usamalola zoweta zako za mitundu yosiyana zikwerane; usamabzala m'munda mwako mbeu za mitundu iwiri; usamabvala cobvala ca nsaru za mitundu iwiri zosokonezana.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 19

Onani Levitiko 19:19 nkhani