Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 19:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musamacita cisalungamo pakuwemza mlandu; usamabvomereza munthu wosauka, kapena kulemekeza munthu womveka; uweruze mlandu wa munthu mnzako molungama.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 19

Onani Levitiko 19:15 nkhani