Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 18:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Usamabvula mkazi ndi mwana wamkazi wace; usamatenga mwana wamkazi wa mwana wamwamuna wace, kapena mwana wamkazi wa mwana wamkazi wace kumbvula; ndiwo abale; cocititsa manyazi ici.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 18

Onani Levitiko 18:17 nkhani