Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 16:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo Aroni aike manja ace onse awiri pamutu pa mbuzi yamoyo, ndi kubvomereza pa iyo mphulupulu zonse za ana a Israyeli, ndi zolakwa zao zonse, monga mwa zocimwa zao zonse; naike izi pamutu pa mbuziyo, ndi kuitumiza kucipululu ndi dzanja la munthu wompangiratu,

Werengani mutu wathunthu Levitiko 16

Onani Levitiko 16:21 nkhani