Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 16:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo Yehova anati kwa Mose, Nena ndi Aroni mbale wako, kuti asalowe nthawi zonse m'malo opatulika m'tseri mwa nsaru yocinga, pali cotetezerapo cokhala palikasa, kuti angafe; popeza ndioneka mumtambo pacotetezerapo.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 16

Onani Levitiko 16:2 nkhani