Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 16:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Aroni abwere nayo ng'ombe ya nsembe yaucimo, ndiyo yace yace, nadzitetezere iye yekha, ndi mbumba yace, ndi kupha ng'ombe ya nsembe yaucimo ndiyo yace yace;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 16

Onani Levitiko 16:11 nkhani