Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 15:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudetsedwa kwa kukha kwace ndiko: ngakhale cakukhaco cituruka m'thupi mwace, ngakhale caleka m'thupi mwace, ndiko kumdetsa kwace.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 15

Onani Levitiko 15:3 nkhani