Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 15:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mkazi akakhala ndi kukha mwazi masiku ambiri, osati masiku a kuoloka kwace, kapena akamakha kupitirira nthawi ya kuoloka kwace; masiku onse cirinkukha comdetsa cace, adzakhala wodetsedwa, monga masiku a kuoloka kwace.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 15

Onani Levitiko 15:25 nkhani