Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 15:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ali yense akhudza cinthu ciri conse akhalapo iye, atsuke zobvala zace, nasambe m'madzi, nadzakhala wodetsedwa kufikira madzulo.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 15

Onani Levitiko 15:22 nkhani