Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 15:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ngati mkazi ali ndi nthenda yakukha, ndi kukha kwace nkwa mwazi m'thupi mwace, akhale padera masiku asanu ndi awiri; ndipo ali yense amkhudza adzakhala wodetsedwa kufikira madzulo.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 15

Onani Levitiko 15:19 nkhani