Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 15:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munthu ali yense akakhudza kanthu kali konse kadali pansi pace adzakhala wodetsedwa kufikira madzulo; ndipo iye wakunyamula zimenezo atsuke zobvala zace, nasambe m'madzi, nadzakhala wodetsedwa kufikira madzulo.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 15

Onani Levitiko 15:10 nkhani