Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 14:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsiku lacisanu ndi ciwiri kudzakhala kuti amete tsitsi lace lonse la pamutu pace, ndi ndebvu zace, ndi nsidze zace, inde amete tsitsi lace lonse; natsuke zobvala zace, nasambe thupi lace ndi madzi, nakhale woyera.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 14

Onani Levitiko 14:9 nkhani