Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 14:55-57 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

55. ndi ya khate la cobvala, ndi la nyumba;

56. ndi yacotupa, ndi yankhanambo, ndi yacikanga;

57. kulangiza tsiku loti cikhala codetsa, ndi tsiku loti cikhala coyera; ici ndi cilamulo ca khate.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 14