Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 14:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akaphere mwana wa nkhosa wamwamuna paja amapherapo nsembe yaucimo, ndi nsembe yopsereza, pa malo popatulika; pakuti monga nsembe yaucimo momwemo nsembe yoparamula, nja wansembe; ndiyo yopatulikitsa.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 14

Onani Levitiko 14:13 nkhani