Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 13:51 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

naone nthenda tsiku lacisanu ndi ciwiri; ngati nthenda yakula pacobvala, ngakhale pamuyaro, kapena pamtsendero, kapena pacikopa, ziri zonse zanchito zopangika ndi cikopa; nthendayo ndiyo khate lofukuta; ndico codetsedwa.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 13

Onani Levitiko 13:51 nkhani