Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 13:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ngati cikanga ciima pomwepo, cosakula pakhungu koma cazimba; ndico cotupa ca kupsya; ndipo wansembe amuche woyera; pakuti ndico cipsera ca kupsya.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 13

Onani Levitiko 13:28 nkhani