Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 13:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo wansembe acione; ndipo taonani, ngati tsitsi la cikanga lasanduka lotuwa, ndipo cioneka cakumba kubzola khungu; pamenepo ndilo khate lobuka m'kupsyamo; ndipo wansembe azimucha wodetsedwa ndi nthenda yakhate.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 13

Onani Levitiko 13:25 nkhani