Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 13:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo taonani, ngati cioneka cakumba kubzola khungu, ndipo tsitsi lace lisanduka lotuwa, pamenepo wansembe amuche wodetsedwa; ndiyo nthenda yakhate yabuka m'cirondamo.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 13

Onani Levitiko 13:20 nkhani