Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 11:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye wakudya kanthu ka mtembo wace azitsuka zobvala zace, nadzakhala wodetsedwa kufikira madzulo; iyenso wakunyamula mtembo wace atsuke zobvala zace, nadzakhala wodetsedwa kufikira madzulo.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 11

Onani Levitiko 11:40 nkhani