Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 11:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kanthu ka mtembo wace kakagwa pa zinthu ziri zonse zidzakhala zodetsedwa; ngakhale mcembo kapena mphika wobvundikika, aziswe; zodetsa izi, muziyese zodetsedwa.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 11

Onani Levitiko 11:35 nkhani