Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 10:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Aroni analankhula ndi Mose, nati, Taonani, lero abwera nayo nsembe yao yaucimo ndi nsembe yao yopsereza pamaso pa Yehova; ndipo zandigwera zotere; ndikadadya nsembe yaucimo lero, kukadakomera kodi pamaso pa Yehova?

Werengani mutu wathunthu Levitiko 10

Onani Levitiko 10:19 nkhani