Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 10:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose ananena ndi Aroni, ndi Eleazara ndi Itamara, ana ace otsala, Tengani nsembe yaufa yotsalira ku nsembe zamoto za Yehova, ndi kuidya yopanda cotupitsa pafupi pa guwa la nsembe; pakuti ndiyo yopatulikitsa;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 10

Onani Levitiko 10:12 nkhani