Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 1:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo aiphe ng'ombeyo pamaso pa Yehova; ndipo ana a Aroni, ansembewo, abwere nao mwazi, nawaze mwaziwo pozungulira pa guwa la nsembe, lokhala pa khoma la cihema cokomanako.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 1

Onani Levitiko 1:5 nkhani