Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Levitiko 1:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nang'ambe mapiko ace osawacotsa konse ai; ndipo wansembeyo aitenthe pa guwa la nsembe, pa nkhuni ziri pamoto; ndiyo nsembe yopsereza, nsembe yamoto, ya pfungo lokoma la kwa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 1

Onani Levitiko 1:17 nkhani