Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Hoseya 7:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti asendera nao mtima wao wakunga ng'anjo ya mkate, pokhala alikulalira; wooca mkate wao agona usiku wonse, m'mawa iyaka ngati moto wa malawi.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 7

Onani Hoseya 7:6 nkhani