Ndipo kudzikuza kwa Israyeli kudzamcitira umboni pamaso pace; cifukwa cace Israyeli ndi Efraimu adzakhumudwa m'mphulupulu mwao; Yudanso adzakhumudwa pamodzi nao.