Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Hoseya 4:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace dziko lidzacita cisoni, ndi ali yense wokhalamo adzalefuka, pamodzi ndi nyama za kuthengo, ndi mbalame za m'mlengalenga; ndi nsomba za m'nyanja zomwe zidzacotsedwa.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 4

Onani Hoseya 4:3 nkhani