Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Hoseya 4:18-19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

18. Cakumwa cao casasa, acita citole kosalekeza; akuru ao akonda manyazi kwambiri.

19. Mphepo yamkulunga m'mapiko ace, ndipo adzacita manyazi cifukwa ca nsembe zao.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 4