Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Hoseya 4:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamwamba pa mapiri aphera nsembe, nafukiza pazitunda, patsinde pa thundu, ndi miniali, ndi mkundi; popeza mthunzi wace ndi wabwino, cifukwa cace ana anu akazi acita citole, ndi apongozi anu acita cigololo.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 4

Onani Hoseya 4:13 nkhani