Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Hoseya 2:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti mai wao anacita cigololo; iye amene anali ndi pakati pa iwo anacita camanyazi; pakuti anati, Ndidzatsata ondikondawo, akundipatsa ine cakudya canga, ndi madzi anga, ubweya wanga, ndi thonje langa, mafuta anga, ndi cakumwa canga.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 2

Onani Hoseya 2:5 nkhani