Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Hoseya 2:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzampatsa minda yace yamphesa kuyambira pomwepo, ndi cigwa ca Akori cikhale khomo la ciyembekezo; ndipo adzabvomereza pomwepo monga masiku a ubwana wace, ndi monga tsiku lokwera iye kuturuka m'dziko la Aigupto.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 2

Onani Hoseya 2:15 nkhani