Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Hoseya 2:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzapasula mipesa yace ndi mikuyu yace, imene adanena, Iyi ndi mphotho yanga anandipatsa ondikondawo; ndipo ndidzaisandutsa thengo, ndi nyama zakuthengo zidzaidya.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 2

Onani Hoseya 2:12 nkhani