Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Hoseya 13:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano aonjeza kucimwa, nadzipangira mafano oyenga a siliva wao, mafano monga mwa nzeru zao, onsewo nchito ya amisiri; anena za iwo, Anthu ophera nsembe apsompsone ana a ng'ombe.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 13

Onani Hoseya 13:2 nkhani