Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Hoseya 12:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Efraimu akudya mphepo, natsata mphepo ya kum'mawa; tsiku lonse acurukitsa mabodza ndi cipasuko, ndipo acita pangano ndi Asuri, natenga mafuta kumka nao ku Aigupto,

Werengani mutu wathunthu Hoseya 12

Onani Hoseya 12:1 nkhani